Mphuziro 7 August 15 2020 KUGAWANA MAU Yesu

  • Slides: 9
Download presentation
Mphuziro 7, August 15, 2020 KUGAWANA MAU

Mphuziro 7, August 15, 2020 KUGAWANA MAU

Yesu anati: “[Mau a Mulungu] Achitira umboni za ine. ” (John 5: 39) Mutu

Yesu anati: “[Mau a Mulungu] Achitira umboni za ine. ” (John 5: 39) Mutu waukulu mu Baibulo ndi Yesu. Ichi ndi chifukwa chimene muli mphamvu. Mulungu wadzionetsera yekha kwa anthu munjira zambiri ndipo Baibulo liri lapadera. Sibuku loti tingowerenga, koma “tidye” (Ezekiele 3: 3). Tilole mau a Mulungu adzadze m’maganizo athu, atisinthe, and atipatse mphamvu kugawana ndi ena mutu wa ukulu mu bukuli; omwe uli, chikondi makhalidwe a Yesu. Kodi Baibulo limadziulula motani za ilo ? Ubwino wa Baibulo Mphamvu yake ya kulenga Kodi tingatani nazo? Kupindula ndi ubwino wake Kukhulupirira malonjezano ake Kugawana ndi ena

UBWINO WA BAIBULO “Mau anu ndiwo nyali ya ku mapazi anga, ndi kuunika kwa

UBWINO WA BAIBULO “Mau anu ndiwo nyali ya ku mapazi anga, ndi kuunika kwa panjira panga. ” (Masalimo 119: 105) Baibulo limayerekezedwa ndi zizindikiro zosiyanasiya kusonyeza makhalidwe ake. Masalimo 119: 105 Yeremiya 23: 29 Kuwala Moto Hamala Maganizo a mdima amapepuka Uchimo umanyekets edwa Mitima youma imasweka Luka 8: 11 Mateyu 4: 4 Limadzala moyo mwaife obala zipatso za ufumu wa Mulungu Limadyetsa ndikukulitsa moyo wathu wauzimu Mbeu Pamene tiwerenga mau a Mulungu, Miyoyo yathu imasinthika ndi ubwino wake, kukopeka ndi chikondi chake, kuzizwa ndi chisomo chake, ndi kukhutitsidwa ndi kupezeka kwake. Nkate

MPHAVU YAKE YAKULENGA “Pakuti mau a Mulungu ali amoyo, ndi ochita, ndi akuthwa koposa

MPHAVU YAKE YAKULENGA “Pakuti mau a Mulungu ali amoyo, ndi ochita, ndi akuthwa koposa lupanga lakuthwa konse, napyoza kufikira kugawira moyo ndi mzimu, ndi zimfundo ndi mafuta a m'mafupa, nazindikiritsa zolingirira ndi zitsimikizo za mtima. ” (Ahebri 4: 12) Pachiyambi, Mulungu “Anayankhula, ndipo chinachitika; Analamula, ndipo chinakhazikika. ” (Masalimo 33: 9) Mphamvu yomweyo ya mawu a Mulungu yakulenga ikupezekanso mu mawu olembedwa, Baibulo. Mzimu womwewo omwe unagwira ntchito pa kulenga unauzilanso malemba ake. Mzimu Woyera ukhonza kutilenganso mwatsopano. Tingofunika timulole angwire nafe ntchito mmene tikuwerenga mawu ake. Mzimu Woyera akhonzanso kusintha anthu ena pamene tiwathandiza kumvetsetsa malemba a Mulungu.

KUPINDULA NDI UBWINO WAKE “Lemba lililonse adaliuzira Mulungu, ndipo lipindulitsa pa chiphunzitso, chitsutsano, chikonzero,

KUPINDULA NDI UBWINO WAKE “Lemba lililonse adaliuzira Mulungu, ndipo lipindulitsa pa chiphunzitso, chitsutsano, chikonzero, chilangizo cha m'chilungamo. ” (2 Timothy 3: 16) Mu Baibulo muli zambiri zopindulitsa miyoyo yathu. Tiyeni tioneko zina zaizo. 2 Petro 1: 4. Kukakhala oyanjana nao umulungu wake Yakobo 1: 21. Kupulumutsa miyoyo yathu Machitidwe 20: 32. Kutipatsa cholowa pakati pawoyeretsedwa 2 Timoteo 3: 15, 17. Kutipatsa nzeru, kutiyenereza, ndi kutikonzetsera kugwira ntchito iliyonse yabwino 2 Timoteo 3: 16. Chiphunzitso. Limaulula choonadi ndikuonetsera bodza Chitsutsano. Limaulula Machimo athu Chikonzero. Limasintha zolakwika zathu Chilangizo. Limaulula chilungamo cha Yesu

KUKHULUPIRIRA MALONJEZANO AKE “Koma Mulungu wanga adzakwaniritsa chosowa chanu chilichonse monga mwa chuma chake

KUKHULUPIRIRA MALONJEZANO AKE “Koma Mulungu wanga adzakwaniritsa chosowa chanu chilichonse monga mwa chuma chake m'ulemerero mwa Khristu Yesu. ” (Afilipi 4: 19) Yesaya 40: 31 Luka 12: 27 -28 Masalimo 91: 11 Mu Baibulo muli malonjezano oposa zikwi zitatu (3, 000). Mulungu ndiokonzeka kukwaniritsa onsewa mu moyo wathu, Akutilimbikitsa kuti tiwatchule malonjezanowa. Amatsimikizira kuti Mulungu amasamalira Yesaya 33: 16 zosowa zathu zaku thupi komanso za uzimu. Yesaya 43: 2 Tsiku lomwe tidzamuone maso ndi maso, tidzanena: “Monga mwa zonse analonjeza, Sanatayike amodzi a mau ake onse abwino. ” (1 Mafumu 8: 56) Koma, Malonjezano ake sakhala opanda malire. Kusowa chikhulupiriro kutha kulepheretsa kuti malonjezano akwanilitsidwe Masalimo 4: 8 (Hebrews 4: 2). Malonjezano a Mulungu amakhala athu pamene tiwalengeza mwa chikhulupiliro chifukwa Khristu Yesu ali okhulupirika.

“Malemba akuyenera kulandiridwa monga mawu a Mulungu kwa ife, osati ngati zolembera chabe, koma

“Malemba akuyenera kulandiridwa monga mawu a Mulungu kwa ife, osati ngati zolembera chabe, koma wouzilidwa […] Kotero ndi Malonjezano ake onse akuyankhula ndi aliyense payekha, kuyankhula mwachindunji ngati tikumvetsera liwu lake. Kupyolera mumalonjezano ake, Khristu akutionetsera chisomo ndi mphamvu zake. Ali monga masamba amtengo uja ‘wakuchiza amitundu. ’ Chivumbulutso 22: 2. Zolandiridwa, zikuyenera kukhala mphamvu ya kudzoza ndi chisamaliro cha moyo. ” E. G. W. (The Ministry of Healing, cp. 7, p. 122)

KUGAWANA NDI ENA “Ambuye Yehova wandipatsa Ine lilime la ophunzira, kuti ndidziwe kunena mau

KUGAWANA NDI ENA “Ambuye Yehova wandipatsa Ine lilime la ophunzira, kuti ndidziwe kunena mau akuchirikiza iye amene ali wolema. Iye andigalamutsa m'mawa ndi m'mawa, nagalamutsa khutu langa kuti limve monga ophunzira. ” (Isaiah 50: 4) Mulungu “amadzutsa” khutu lathu ndi kupereka nzeru pamene tikuwerenga baibulo tsiku ndi tsiku. Amatipatsanso “lilime la ophunzira” kuti tiphunzitse ena za mau ake. Mau a Mulungu sitingawatsekere mkati mwa mitima yathu. Chisangalalo cha chipulumutso chimatikakamiza ife kugawa uthenga wake ndi iwo amene sakuuziwa. Paulo anatilangiza kuti: “Lalika uthenga; chita nawo panthawi yake; tsutsa, dzudzula, chenjeza —ndi kuleza mtima konse ndi chiphunzitso. ” (2 Timoteo 4: 2)

“The education to be secured by searching the Scriptures is an experimental knowledge of

“The education to be secured by searching the Scriptures is an experimental knowledge of the plan of salvation. Such an education will restore the image of God in the soul. It will strengthen and fortify the mind against temptation, and fit the learner to become a co-worker with Christ in His mission of mercy to the world. It will make him a member of the heavenly family; and prepare him to share the inheritance of the saints in light. ” E. G. W. (Christ’s Object Lessons, cp. 2, p. 42)